Zaka Za Pitazo

Phungu Joseph Nkasa

Zaka Zapitazo mubuku lamwamba
Ndinari mukongoli yazoimba zanga
imo dzina ranga lina lembedwako
Ndinazo kwawalembayo ndalikana ndiayo

Ngongoni inakura yasiku ndi siku
wakuti Wochimwa
wosaripirazo koma poyangana
Zowawa tsogoro ndati ndizalipila
Malipo oyangana

Tembenuka iwe Tembenuka ima Tembenuka ntawi yata X2

Usana mwalile pfunza mwoyo wako
Chitambo chenjera sema kuchena
Ulendo wakumwamba woyenda ndimutima
Chenjera ungati njoka uratizo
Njoka inachejerera kupaza mwoyo zose
Kolowa hakuna isogo zamutu tupiri sanate zose
iTembenuza mutu yo Kuyangana kupumo
Gwira njira imodzi
Tembenuka iwe Tembenuka ima Tembenuka ntawi yata X2


Ndimakonda kwambiri ndapunzisa nzeru
peche peceh
Zapita kawiri Ndikubwerozonse
Kuonesa mwano emery osamvera anandipa ndimkango
Zinje ndikanena sanaterere Tsitsi
Kusanena

Muntu wachimwira zake pasi pano
Mai anaweruza asayanjanisa
Koma akamwira ndihehova

Paulendo wamwamba uwu
Uselege mwana anu
agare patsogoro akulu pambuyo
Chomwe munaziwe ufumu wamulungu
Ana ukazikise pakati pakiwana
Usakonjele pano sana usafike
sona watopa
Kutuluka zuwa
napinda amupaladiso
Tembenuka iwe Tembenuka ima Tembenuka ntawi yata X2

Lyrics Submitted by Love Must

Lyrics provided by https://damnlyrics.com/