A Phiri Anabwera

Nashil Pichen Kazembe

(first two verses only)
Aphiri anabwela kuchoka ku Harare
Anakhalako dzaka zosawelengeka ndithu
Pobwera kumuzi anabwela ndi situkesi
Mukati mwasutukezi munalibe kantu sure

Kumuzi anapeza makozo anaamwalila
Panalibe muntu aliyinse angawadziwe
Anayangana m'mwamba anayangana pansi

Lyrics Submitted by Achimwene

Lyrics provided by https://damnlyrics.com/