Mundikumbuke amayi ndasara ndekha,
Mundikumbuke amayi ndasara ndekha ine,
Mundikumbuke amayi ndasara ndekha.
Mundikumbuke amayi ndasara ndekha.
Mundikumbuke amayi ndasara ndekha.
Mundikumbuke amayi ndasara ndekhaaaaa.
Amayi asanafe, anasiya mau.
Amayi asanafe eeh, anasiya mau.
Usafunefune moyenda bambo ulinawo.
Usafunefune moyenda bambo ulinawo.
Usafunefune moyenda bambo ulinawo.
Usafunefune moyenda bambo ulinawooooo.
Ndine mwana wapatchire, okula ndi amayi.
Ndine mwana wapatchire ine, okula ndi amayi.
Ndine mwana wamasiye, okulira mu umphawi.
Ndine mwana wamasiye, okulira mu umphawi.
Ndine mwana wamasiye ine, okulira mu umphawi.
Ndine mwana wamasiye ine, okulira mu umphawiiiii.
Azimayi achiwiri, ana amasiye.
Mverani.
Azimayi achiwiri, ana amasiye.
Apatsopeni, monga ana anuso.
Apatsopeni, monga ana anuso.
Osataya.
Apatsopeni eeh, monga ana anuso.
Apatsopeni eeh, monga ana anuso.
Chifundo!
Ndili ndi chifundo ine.
Chifundo!
Ndili ndi chifundo ine.
Mavuto!
Ndili ndi mavuto ine.
Mavuto!
Ndili ndi mavuto ine.
Amayi anandilera,anamwalira kale.
Amayi anandilera ine, anamwalira kale.
Poyenda ndimangolira, kukumbuka ondibala.
Poyenda ndimangolira ine, kukumbuka ondibara.
Pogona ndi misonzi chabe, bambo anga muli kuti inu.
Pogona ndi misonzi chabe, bambo anga muli kuti inu.
Ndakulira mu umphawi, opanda chisoni ndithu.
Ndakulira mu umphawi, opanda chisoni ndithu.
Ngati muli ndi umoyo, kapena munamwalira.
Ngati mili ndi umoyo, kapena munamwalira.
Bwanji osabwera Ku tulo, kapena ndingakondwereko.
Bwanji osabwera Ku tulo, kapena ndingakondwereko.
Chifundo!
Ndili ndi chifundo ine.
Chifundo!
Ndili ndi chifundo ine.
Mavuto!
Ndili ndi mavuto ine.
Mavuto!
Ndili ndi mavuto ine.
Achisale!
Mwayenela!
Mayooo! Mayooo!