damnlyrics.com

Nsokoto

Kumsokoto kuli mfiti imodzi inkalodza ana osalakwa

Kupata kwa ana iyo sinkasangalatsidwa nako

Mwana apate eti tiona ngati agoneChaka chino chokha iye akagonera kumandaM'mati n'kwere ndakwera panyumba yanthakati

Wakoma bana pawaka

Wamara bana nsokotoMwana akangoti agone

Kum'bwerera usiku

Thupi lonse lamangika

Kulephera kufuula

Poti adsuke mam'mawa

Thupi kunjenjemera

Mutu wanga, malungo, matenda aja akula

Wakoma bana

Wati kitasha

Wamara bana

Ichi n'chasoniNsokoto nsokoto

Nsokoto nsokotoMuuze nthakatiyo namulondola ife takana

Bana bakunsokoto ise

Bana bakumulowe ise

Bana bamwakisulu ise

Bana bakaronga ise

Bana bakurumphi ise

Bana bakuchitipa ise

Song Discussions is protected by U.S. Patent 9401941. Other patents pending.

Enjoy the lyrics !!!