A Phiri Anabwera - Nashil Pichen Kazembe



     
Page format: Left Center Right
Direct link:
BB code:
Embed:

A Phiri Anabwera Lyrics


(first two verses only)
Aphiri anabwela kuchoka ku Harare
Anakhalako dzaka zosawelengeka ndithu
Pobwera kumuzi anabwela ndi situkesi
Mukati mwasutukezi munalibe kantu sure
Kumuzi anapeza makozo anaamwalila
Panalibe muntu aliyinse angawadziwe
Anayangana m'mwamba anayangana pansi
Lyrics Submitted by Achimwene

Enjoy the lyrics !!!