Chauta ndi Wamphamvu - Evison Matafale
| Page format: |
Chauta ndi Wamphamvu Lyrics
Instrumentals(19 sec)
Verse1
Ukaona dzuwa latulukaa!
Mbalaame nazo ziku zikuyimbaa
Chauta wa mphamvu,Chauta ngwamphavu.
(*Repeat above*)
Chauta ngwamphavu,Chauta ngwamphavu
Chorus
Amatigonetsaa kukada!
Amatidzutsa kukacha
Amatidyetsaa tikamva njala!
Amatisaka tikataika
Amatichizaa tikadwala!
Amativeka tikasauka
Tipempheree kuti iziii pitilire
Timtamande kuti iye asasiye
Ukaona dzuwa latulukaa!
Mbalaame nazo zikuyimba
Chauta ngwamphavu,Chauta ngwamphavu
Instrumentals(30sec)
Verse2
Ukaona mwezi wawalaa!
Nkumaamvaso ana akusewera
Chauta ngwamphavu,chauta waamphamvu
(Repeat above)
Chauta wamphamvu,chauta wamphamvu
Chorus
Amatigonetsaa kukada!
Amatidzutsa kukacha
Amatidyetsaa tikamva njala!
Amativeka tikasauka
Amatisakaa tikataika!
Amativeka tikasauka
Tipempheree kuti izii pitilire
Timtamande kuti iye asasiyee
Ukaona mwezi wawala!
Nkumaavaso ana akusewera
Chauta wamphamvu,chauta ndi wamphamvu
Instrumentals
Chorus
Amatigonetsaa kukada!
Amatidzutsa kukacha
Amatidyetsaa tikamva njala!
Amatichiza tikadwala
Amatisaaka tikataika
Amatichiza tikadwala
Lyrics Submitted by Fatsani Rose Manase