Olakwa ndani - Evison Matafale
| Page format: |
Olakwa ndani Lyrics
olakwa ndani!,olakwa ndani,olakwa ndani,olakwa ndani
(repeat)
instrumentals
Mtima wanga ine!
Mzimu wanga Ine!
Nzeru zanga ineee
Zasaukaa.
Ndikamayenda!
ntown ine!
Ndimati ndi ndekhaa!
ovutika
ndikamayenda!
eeh ntown ine
ndimati ndi ndekha!
ovutika
Koma ena alibe!
ngakhale pogona(with vocalists)
umphawi wa dzaone!
Dziko Ili
ndati ena alibe!
ngakhale chovala(with vocalist)
umphawi wa dzaone
Mdziko ili
koma,
olakwa ndani!,olakwa ndani,olakwa ndani,olakwa ndani(repeat)
verse2
Walira mnyamata!
dziko la chilendo!
Kodi mdapha ndani ine
Kuti nteree
woyankha nkumati!
usalire iwe
Dziko laa pansi ndilotero
Oyankha nkumati
eh usalire iwe
dziko laa pansi ndilotero
Umphawi palibe!
amaugonjetsa(with vocalists)
umagonjetsedwa
ndi akufa(repeat)
koma,
olakwa ndani!,olakwa ndani,olakwa ndani,olakwa ndani(repeat)
instruments
verse 3

Lyrics Submitted by Fatsani Rose Manase